Salimo 80:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, chonde bwererani. Yangʼanani pansi pano muli kumwambako kuti muone, Ndipo samalirani mtengo wa mpesa uwu,+
14 Inu Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, chonde bwererani. Yangʼanani pansi pano muli kumwambako kuti muone, Ndipo samalirani mtengo wa mpesa uwu,+