Salimo 82:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mupitiriza kuweruza mopanda chilungamo+Komanso kukondera anthu oipa mpaka liti?+ (Selah)