Salimo 85:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munakhululukira anthu anu zolakwa zawo.Munawakhululukira* machimo awo onse.+ (Selah)