Salimo 85:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tisonyezeni chikondi chanu chokhulupirika inu Yehova,+Ndipo mutipulumutse.