Salimo 85:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, tisonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndipo tipatseni chipulumutso chanu.+