Salimo 109:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndithandizeni, inu Yehova Mulungu wanga.+Ndipulumutseni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+