Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 119:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Monga mwa mawu anu, inu Yehova, ndipatseni chipulumutso chanu.+Ndipatseni zochita zanu zosonyeza kukoma mtima kosatha,+
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
41 Monga mwa mawu anu, inu Yehova, ndipatseni chipulumutso chanu.+Ndipatseni zochita zanu zosonyeza kukoma mtima kosatha,+