Salimo 119:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndione chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova,+Komanso mundipulumutse mogwirizana ndi lonjezo lanu.*+
41 Ndione chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova,+Komanso mundipulumutse mogwirizana ndi lonjezo lanu.*+