Salimo 119:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Monga mwa mawu anu, inu Yehova, ndipatseni chipulumutso chanu.+Ndipatseni zochita zanu zosonyeza kukoma mtima kosatha,+
41 Monga mwa mawu anu, inu Yehova, ndipatseni chipulumutso chanu.+Ndipatseni zochita zanu zosonyeza kukoma mtima kosatha,+