Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+

      Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+

  • Salimo 85:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Yehova, tisonyezeni kukoma mtima kwanu kosatha,+

      Ndipo tipatseni chipulumutso chanu.+

  • Salimo 90:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 M’mawa mutikhutiritse ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+

      Kuti tifuule mokondwera ndi kuti tikhale osangalala masiku onse a moyo wathu.+

  • Salimo 106:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndikumbukireni inu Yehova, ndipo ndisonyezeni kukoma mtima kumene mumasonyeza anthu anu.+

      Ndisamalireni ndi kundipulumutsa,+

  • Salimo 119:76
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  76 Kukoma mtima kwanu kosatha kundilimbikitse,+

      Monga mwa mawu anu kwa ine mtumiki wanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena