Salimo 86:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sangalatsani mtima wa ine mtumiki wanu,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu Yehova.+ Salimo 149:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Isiraeli asangalale ndi Womupanga Wamkulu,+Ana a Ziyoni akondwere ndi Mfumu yawo.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+