Salimo 119:76 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 76 Chikondi chanu chokhulupirika+ chindilimbikitse,Mogwirizana ndi zimene munandilonjeza* ine mtumiki wanu. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:76 Nsanja ya Olonda,8/15/2010, tsa. 24
76 Chikondi chanu chokhulupirika+ chindilimbikitse,Mogwirizana ndi zimene munandilonjeza* ine mtumiki wanu.