Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+ Salimo 86:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova ndinu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Mumasonyeza chikondi chokhulupirika chochuluka kwa onse amene amaitana inu.+
6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+
5 Inu Yehova ndinu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Mumasonyeza chikondi chokhulupirika chochuluka kwa onse amene amaitana inu.+