Genesis 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu ndidzayembekezera chipulumutso kwa inu, Yehova.+ Salimo 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+ Luka 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa maso anga aona njira yanu yopulumutsira+
7 Haa! Zikanakhala bwino m’Ziyoni mukanapezeka chipulumutso cha Isiraeli.+Yehova akadzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu ake amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+Yakobo adzasangalale, Isiraeli adzakondwere.+