Salimo 88:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anzanga komanso anthu oyandikana nawo mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Malo amdima akhala mnzanga wapamtima.
18 Anzanga komanso anthu oyandikana nawo mwawathamangitsira kutali ndi ine.+Malo amdima akhala mnzanga wapamtima.