Salimo 119:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndimakufunafunani ndi mtima wanga wonse. Musalole kuti ndisochere nʼkuchoka pa malamulo anu.+