Salimo 119:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndayesetsa kukufunafunani ndi mtima wanga wonse.+Musandichititse kusochera ndi kuchoka pa malamulo anu.+
10 Ndayesetsa kukufunafunani ndi mtima wanga wonse.+Musandichititse kusochera ndi kuchoka pa malamulo anu.+