Salimo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+ Salimo 119:118 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+
5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+
118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+