Salimo 119:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndithandizeni kumvetsa tanthauzo la* malamulo anu,Kuti ndiganizire mozama* ntchito zanu zodabwitsa.+
27 Ndithandizeni kumvetsa tanthauzo la* malamulo anu,Kuti ndiganizire mozama* ntchito zanu zodabwitsa.+