Salimo 119:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndithandizeni kumvetsa njira zofotokozedwa m’malamulo anu,+Kuti ndisinkhesinkhe ntchito zanu zodabwitsa.+
27 Ndithandizeni kumvetsa njira zofotokozedwa m’malamulo anu,+Kuti ndisinkhesinkhe ntchito zanu zodabwitsa.+