Salimo 103:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+ Salimo 119:94 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Ine ndine wanu. Chonde ndipulumutseni,+Chifukwa ndaphunzira malamulo anu ndi kuwasunga.+
18 Adzapitiriza kuchita zimenezi kwa anthu osunga pangano lake,+Ndi kwa anthu okumbukira malamulo ake ndi kuwatsatira.+