Salimo 119:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzasinkhasinkha malamulo anu,+Ndipo ndidzalabadira njira zanu.+ Salimo 119:168 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 168 Ndasunga malamulo anu ndi zikumbutso zanu,+Pakuti njira zanga zonse zili pamaso panu.+