Salimo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+ Salimo 139:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+ Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+
3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+
11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+