Salimo 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye akuumba mtima wa aliyense wa iwo.+Akulingalira ntchito zawo zonse.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+ Yesaya 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+ Machitidwe 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Petulo anati: “Hananiya, n’chifukwa chiyani Satana+ wakulimbitsa mtima choncho kuti uyese kunamiza+ mzimu woyera+ ndi kubisa zina mwa ndalama za mtengo wa mundawo?
15 Tsoka kwa anthu amene abisa patali kwambiri zolinga zawo, pozibisira Yehova,+ amene zochita zawo zimachitikira m’malo a mdima,+ ndipo amati: “Ndani akutiona, ndipo ndani akudziwa zimene tikuchita?”+
3 Koma Petulo anati: “Hananiya, n’chifukwa chiyani Satana+ wakulimbitsa mtima choncho kuti uyese kunamiza+ mzimu woyera+ ndi kubisa zina mwa ndalama za mtengo wa mundawo?