Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+ Machitidwe 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Petulo anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese+ mzimu wa Yehova? Taona! Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako m’manda ali pakhomo. Iwenso akunyamula ndi kutuluka nawe.”
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
9 Pamenepo Petulo anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese+ mzimu wa Yehova? Taona! Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako m’manda ali pakhomo. Iwenso akunyamula ndi kutuluka nawe.”