1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni,+ muimbireni nyimbo zomutamanda!+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ 2 Mbiri 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+ Salimo 105:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muimbireni, muimbireni nyimbo zomutamanda,+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Salimo 145:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzasinkhasinkha za ulemerero wanu waukulu+Ndi nkhani zokhudza ntchito zanu zodabwitsa.+
22 Chotero, Yehova anapulumutsa Hezekiya ndi anthu okhala ku Yerusalemu m’manja mwa Senakeribu mfumu ya Asuri+ komanso m’manja mwa ena onse, ndipo anawapatsa mpumulo kwa adani awo onse owazungulira.+