Salimo 119:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndimatsatira zikumbutso zanu nthawi zonse.+ Inu Yehova, musalole kuti ndikhumudwe.*+