Salimo 119:119 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Anthu onse oipa apadziko lapansi mumawataya ngati zinthu zopanda ntchito zimene zimatsalira poyenga zitsulo.+ Nʼchifukwa chake ine ndimakonda zikumbutso zanu. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:119 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 28
119 Anthu onse oipa apadziko lapansi mumawataya ngati zinthu zopanda ntchito zimene zimatsalira poyenga zitsulo.+ Nʼchifukwa chake ine ndimakonda zikumbutso zanu.