Salimo 131:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 131 Inu Yehova, mtima wanga si wodzikweza,Maso anga si onyada.+Sindilakalaka zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zimene sindingazikwanitse. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 131:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2021, tsa. 22
131 Inu Yehova, mtima wanga si wodzikweza,Maso anga si onyada.+Sindilakalaka zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zimene sindingazikwanitse.