Salimo 140:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wonenera anzake zoipa asapeze malo padziko lapansi.*+ Zoipa zisakesake anthu ochita zachiwawa ndipo ziwawononge.
11 Munthu wonenera anzake zoipa asapeze malo padziko lapansi.*+ Zoipa zisakesake anthu ochita zachiwawa ndipo ziwawononge.