Salimo 140:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wolankhula zazikulu* asakhazikike padziko lapansi.+Zoipa zisakesake munthu wochita zachiwawa ndipo zimukanthe mobwerezabwereza.+
11 Munthu wolankhula zazikulu* asakhazikike padziko lapansi.+Zoipa zisakesake munthu wochita zachiwawa ndipo zimukanthe mobwerezabwereza.+