Miyambo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amatamandidwa chifukwa cholankhula zinthu zanzeru,+Koma amene ali ndi mtima wopotoka adzanyozedwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, tsa. 30 Sukulu ya Utumiki, tsa. 198
8 Munthu amatamandidwa chifukwa cholankhula zinthu zanzeru,+Koma amene ali ndi mtima wopotoka adzanyozedwa.+