Miyambo 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amanyansidwa ndi njira ya munthu woipa,+Koma amakonda munthu amene amachita chilungamo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:9 Nsanja ya Olonda,7/1/2006, tsa. 15