Miyambo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mphatso ili ngati mwala wamtengo wapatali kwa mwiniwake.*+Kulikonse kumene wapita, imachititsa kuti zinthu zimuyendere bwino.+
8 Mphatso ili ngati mwala wamtengo wapatali kwa mwiniwake.*+Kulikonse kumene wapita, imachititsa kuti zinthu zimuyendere bwino.+