Miyambo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mawu amʼkamwa mwa munthu ali ngati madzi akuya.+ Kasupe wa nzeru ali ngati mtsinje wosefukira.