Miyambo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wonyoza akapatsidwa chilango, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru,Ndipo munthu wanzeru akaphunzira zinthu zambiri, amadziwa zinthu.*+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:11 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 29
11 Munthu wonyoza akapatsidwa chilango, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru,Ndipo munthu wanzeru akaphunzira zinthu zambiri, amadziwa zinthu.*+