Miyambo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa kulipiritsa munthu wonyoza, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru.+ Munthu wanzeru akapatsidwa malangizo, amadziwa zinthu.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:11 Nsanja ya Olonda,6/1/1988, tsa. 29
11 Mwa kulipiritsa munthu wonyoza, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru.+ Munthu wanzeru akapatsidwa malangizo, amadziwa zinthu.+