Miyambo 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhani yabwino yochokera kudziko lakutali+Ili ngati madzi ozizira kwa munthu wotopa.