Miyambo 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usasiye mnzako kapena mnzawo wa bambo ako,Ndipo usalowe mʼnyumba ya mchimwene wako pa tsiku limene tsoka lakugwera.Munthu woyandikana naye nyumba amene ali pafupi ali bwino kuposa mchimwene wako amene ali kutali.+
10 Usasiye mnzako kapena mnzawo wa bambo ako,Ndipo usalowe mʼnyumba ya mchimwene wako pa tsiku limene tsoka lakugwera.Munthu woyandikana naye nyumba amene ali pafupi ali bwino kuposa mchimwene wako amene ali kutali.+