Miyambo 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+ Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali anthu ogwirizana amene ndi okonzeka kuchitirana zoipa,+Koma pali mnzako amene amakhala nawe pafupi nthawi zonse kuposa mʼbale wako.+
17 Mnzako weniweni amakusonyeza chikondi nthawi zonse,+Ndipo ndi mʼbale amene anabadwa kuti akuthandize pakagwa mavuto.+
24 Pali anthu ogwirizana amene ndi okonzeka kuchitirana zoipa,+Koma pali mnzako amene amakhala nawe pafupi nthawi zonse kuposa mʼbale wako.+