Miyambo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu akapereka moni kwa mnzake* mokuwa mʼmamawa kwambiri,Mnzakeyo sangasangalale nazo.*