Miyambo 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amene amadalitsa mnzake mokuwa m’mawa kwambiri, anthu adzamuona ngati akutemberera.+