Miyambo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhala mʼdziko akamachimwa,* dzikolo limasintha akalonga pafupipafupi,+Koma kalonga akamathandizidwa ndi munthu wozindikira komanso wodziwa zinthu, amakhala nthawi yaitali.+
2 Anthu okhala mʼdziko akamachimwa,* dzikolo limasintha akalonga pafupipafupi,+Koma kalonga akamathandizidwa ndi munthu wozindikira komanso wodziwa zinthu, amakhala nthawi yaitali.+