Mlaliki 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitseko zotulukira popita mumsewu zidzatsekedwa, phokoso la miyala yoperera ufa lidzayamba kumveka motsika ndipo munthu azidzadzuka ndi kulira kwa mbalame, ndiponso ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mawu ofooka.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,11/2016, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/15/1999, ptsa. 15-16
4 Zitseko zotulukira popita mumsewu zidzatsekedwa, phokoso la miyala yoperera ufa lidzayamba kumveka motsika ndipo munthu azidzadzuka ndi kulira kwa mbalame, ndiponso ana onse aakazi azidzaimba nyimbo ndi mawu ofooka.+
12:4 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,11/2016, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/15/1999, ptsa. 15-16