Mlaliki 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wosonkhanitsa anthu akunena kuti:+ “Nʼzachabechabe!* Zinthu zonse nʼzachabechabe.”+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda,11/15/1999, ptsa. 18-19