Nyimbo ya Solomo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nditangowapitirira pangʼono,ndinamʼpeza munthu amene ndimamukonda. Ndinamugwira ndipo sindinafune kumʼsiyaMpaka nditamubweretsa mʼnyumba ya mayi anga,+Mʼchipinda chamkati cha mayi amene anali ndi pakati kuti ine ndibadwe.
4 Nditangowapitirira pangʼono,ndinamʼpeza munthu amene ndimamukonda. Ndinamugwira ndipo sindinafune kumʼsiyaMpaka nditamubweretsa mʼnyumba ya mayi anga,+Mʼchipinda chamkati cha mayi amene anali ndi pakati kuti ine ndibadwe.