-
Nyimbo ya Solomo 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Nditangowapitirira pang’ono, ndinam’peza munthu amene mtima wanga umam’konda. Ndinamugwira ndipo sindinafune kum’siya mpaka nditamubweretsa m’nyumba mwa mayi anga, m’chipinda chamkati cha mayi amene anali ndi pakati kuti ine ndibadwe.
-