-
Nyimbo ya Solomo 7:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “Mapazi ako akukongola kwambiri munsapato zako,
Iwe mwana wamkazi wolemekezeka.
Ntchafu zako nʼzoumbidwa bwino ngati zinthu zodzikongoletsera,
Ntchito ya manja a munthu waluso.
-