Nyimbo ya Solomo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Mapazi ako akukongola kwambiri munsapato zako,+ iwe mwana wamkazi+ wodzipereka. Ntchafu zako n’zoumbidwa bwino ngati zinthu zokongoletsera,+ ngati ntchito ya manja a munthu waluso.
7 “Mapazi ako akukongola kwambiri munsapato zako,+ iwe mwana wamkazi+ wodzipereka. Ntchafu zako n’zoumbidwa bwino ngati zinthu zokongoletsera,+ ngati ntchito ya manja a munthu waluso.