Nyimbo ya Solomo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mutu wako ndi wokongola ngati phiri la Karimeli,+Ndipo tsitsi lako lopotanapotana+ lili ngati ubweya wa nkhosa wapepo.+ Mfumu yakopeka* ndi tsitsi lako lalitali lokongolalo. Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Nsanja ya Olonda,8/15/1996, tsa. 7
5 Mutu wako ndi wokongola ngati phiri la Karimeli,+Ndipo tsitsi lako lopotanapotana+ lili ngati ubweya wa nkhosa wapepo.+ Mfumu yakopeka* ndi tsitsi lako lalitali lokongolalo.